Aheberi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zinthu zonse munaziika pansi pa mapazi ake.”+ Popeza kuti anaika zinthu zonse pansi pa mwana wake,+ Mulungu sanasiye kanthu kalikonse, osakaika pansi pa mwana wakeyo.+ Komabe, padakali pano sitikuona kuti zinthu zonse zili pansi pake.+
8 Zinthu zonse munaziika pansi pa mapazi ake.”+ Popeza kuti anaika zinthu zonse pansi pa mwana wake,+ Mulungu sanasiye kanthu kalikonse, osakaika pansi pa mwana wakeyo.+ Komabe, padakali pano sitikuona kuti zinthu zonse zili pansi pake.+