Yohane 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso m’Chilamulo chanu chomwechi analembamo kuti, ‘Umboni wa anthu awiri ndi woona.’+