Yesaya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imvani mawu a Yehova,+ inu olamulira ankhanza+ a ku Sodomu.+ Mvetserani malamulo a Mulungu wathu, inu anthu a ku Gomora.
10 Imvani mawu a Yehova,+ inu olamulira ankhanza+ a ku Sodomu.+ Mvetserani malamulo a Mulungu wathu, inu anthu a ku Gomora.