Yesaya 66:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kodi ine ndingachititse kuti chiberekero chitseguke koma osachititsa kuti mwana abadwe?”+ akutero Yehova. “Kapena kodi ndingachititse kuti mwana atsale pang’ono kubadwa kenako n’kutseka chiberekero?” watero Mulungu wanu.
9 “Kodi ine ndingachititse kuti chiberekero chitseguke koma osachititsa kuti mwana abadwe?”+ akutero Yehova. “Kapena kodi ndingachititse kuti mwana atsale pang’ono kubadwa kenako n’kutseka chiberekero?” watero Mulungu wanu.