Luka 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno iye anawauza kuti: “Ndinayamba kuona Satana atagwa+ kale ngati mphezi kuchokera kumwamba. Chivumbulutso 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano chinjoka chitaona kuti achigwetsera kudziko lapansi,+ chinazunza mkazi+ amene anabereka mwana wamwamuna uja.
13 Tsopano chinjoka chitaona kuti achigwetsera kudziko lapansi,+ chinazunza mkazi+ amene anabereka mwana wamwamuna uja.