Salimo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zingwe za imfa zinandikulunga,+Chikhamu cha anthu opanda pake chinali kundiopseza.+ Yesaya 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsoka kwa mitundu ya anthu ambirimbiri amene akuchita chipwirikiti, amene akuwinduka ngati nyanja. Tsoka kwa magulu a mitundu ya anthu aphokoso, amene akusokosera ngati mkokomo wa madzi amphamvu.+
12 Tsoka kwa mitundu ya anthu ambirimbiri amene akuchita chipwirikiti, amene akuwinduka ngati nyanja. Tsoka kwa magulu a mitundu ya anthu aphokoso, amene akusokosera ngati mkokomo wa madzi amphamvu.+