Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 38:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ine ndinati: “Pakatikati pa masiku anga ndidzalowa pazipata+ za Manda.

      Ndidzamanidwa zaka zanga zotsala.”+

  • Mateyu 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero inenso ndikukuuza kuti, Iwe ndiwe Petulo,+ ndipo pathanthwe+ ili ndidzamangapo mpingo wanga. Zipata za Manda+ sizidzaugonjetsa.+

  • Yohane 6:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Wakudya mnofu wanga ndi kumwa magazi anga ali nawo moyo wosatha, ndipo ndidzamuukitsa+ kwa akufa tsiku lomaliza.

  • Yohane 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira mwa ine, ngakhale amwalire, adzakhalanso ndi moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena