Aroma 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kapena simudziwa kuti tonsefe amene tinabatizidwa ndipo tsopano tili mu mgwirizano ndi Khristu Yesu+ tinabatizidwanso mu imfa yake?+ 1 Akorinto 15:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Tamverani! Ndikukuuzani chinsinsi chopatulika: Si tonse amene tidzagona mu imfa, koma tonse tidzasandulika,+
3 Kapena simudziwa kuti tonsefe amene tinabatizidwa ndipo tsopano tili mu mgwirizano ndi Khristu Yesu+ tinabatizidwanso mu imfa yake?+
51 Tamverani! Ndikukuuzani chinsinsi chopatulika: Si tonse amene tidzagona mu imfa, koma tonse tidzasandulika,+