Chivumbulutso 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chilombocho chinakakamiza anthu onse,+ olemekezeka ndi onyozeka, olemera ndi osauka, mfulu ndi akapolo, kuti apatsidwe chizindikiro padzanja lawo lamanja kapena pamphumi pawo.+ Chivumbulutso 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Apa ndiye pofunika nzeru: Amene ali ndi nzeru awerengere nambala ya chilombocho, pakuti ndi nambala ya munthu.+ Nambala yake ndi 666.+
16 Chilombocho chinakakamiza anthu onse,+ olemekezeka ndi onyozeka, olemera ndi osauka, mfulu ndi akapolo, kuti apatsidwe chizindikiro padzanja lawo lamanja kapena pamphumi pawo.+
18 Apa ndiye pofunika nzeru: Amene ali ndi nzeru awerengere nambala ya chilombocho, pakuti ndi nambala ya munthu.+ Nambala yake ndi 666.+