Chivumbulutso 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Apa m’pamene pakufunika kuchenjera ndiponso kukhala ndi nzeru:+ Mitu 7+ ikuimira mapiri 7,+ amene mkazi uja amakhala pamwamba pake.
9 “Apa m’pamene pakufunika kuchenjera ndiponso kukhala ndi nzeru:+ Mitu 7+ ikuimira mapiri 7,+ amene mkazi uja amakhala pamwamba pake.