Mateyu 27:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumeneko anamuvula zovala zake ndi kumuveka chinsalu chofiira kwambiri.+