Aroma 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mulungu amene amapatsa mtendere+ aphwanya Satana+ pansi pa mapazi anu posachedwapa. Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu kukhale ndi inu.+
20 Mulungu amene amapatsa mtendere+ aphwanya Satana+ pansi pa mapazi anu posachedwapa. Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu kukhale ndi inu.+