Mateyu 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo inatuma akapolo ake kuti akaitane anthu oitanidwa ku phwando laukwati,+ koma anthuwo sanafune kubwera.+ Luka 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nthawi ya chakudya chamadzulocho itakwana, anatumiza kapolo wake kukauza oitanidwawo kuti, ‘Tiyeni,+ chifukwa zonse zakonzedwa tsopano.’
3 Ndipo inatuma akapolo ake kuti akaitane anthu oitanidwa ku phwando laukwati,+ koma anthuwo sanafune kubwera.+
17 Nthawi ya chakudya chamadzulocho itakwana, anatumiza kapolo wake kukauza oitanidwawo kuti, ‘Tiyeni,+ chifukwa zonse zakonzedwa tsopano.’