Chivumbulutso 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chilombocho chinalamulira ndi mphamvu zonse za chilombo choyambacho+ pamaso pa chilombo choyambacho. Chinachititsa dziko lapansi ndi okhalamo kulambira chilombo choyamba chija, chimene bala lake limene chinayenera kufa nalo, linapola.+
12 Chilombocho chinalamulira ndi mphamvu zonse za chilombo choyambacho+ pamaso pa chilombo choyambacho. Chinachititsa dziko lapansi ndi okhalamo kulambira chilombo choyamba chija, chimene bala lake limene chinayenera kufa nalo, linapola.+