2 Akorinto 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene iwo anali kuyesedwa kwambiri chifukwa cha mavuto, anali achimwemwe kwambiri ndiponso anasonyeza kuwolowa manja kwakukulu, ndipo anachita zimenezi ngakhale kuti anali pa umphawi wadzaoneni.+ Aheberi 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Popeza kuti iye mwini anavutika pamene anali kuyesedwa,+ amatha kuthandiza anthu amene akuyesedwa.+
2 Pamene iwo anali kuyesedwa kwambiri chifukwa cha mavuto, anali achimwemwe kwambiri ndiponso anasonyeza kuwolowa manja kwakukulu, ndipo anachita zimenezi ngakhale kuti anali pa umphawi wadzaoneni.+
18 Popeza kuti iye mwini anavutika pamene anali kuyesedwa,+ amatha kuthandiza anthu amene akuyesedwa.+