Miyambo 8:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene ankakonza kumwamba, ine ndinali pomwepo.+Pamene ankaika malire pakati pa mlengalenga ndi nyanja,+28 Pamene ankakhazikitsa* mitambo kumwamba,Pamene ankakhazikitsa akasupe a madzi akuya,
27 Pamene ankakonza kumwamba, ine ndinali pomwepo.+Pamene ankaika malire pakati pa mlengalenga ndi nyanja,+28 Pamene ankakhazikitsa* mitambo kumwamba,Pamene ankakhazikitsa akasupe a madzi akuya,