Genesis 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuti ndipezeke kuno anachita kundiba kudziko la Aheberi,+ ndipo palibe chilichonse chimene ndinalakwa choti andiikire mʼndende* muno.”+
15 Kuti ndipezeke kuno anachita kundiba kudziko la Aheberi,+ ndipo palibe chilichonse chimene ndinalakwa choti andiikire mʼndende* muno.”+