Genesis 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Mulungu analenga munthu mʼchifaniziro chake, mʼchifaniziro cha Mulungu analenga munthu. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+ Maliko 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma kuyambira pachiyambi pa chilengedwe, ‘Mulungu anawalenga mwamuna ndi mkazi.+
27 Choncho Mulungu analenga munthu mʼchifaniziro chake, mʼchifaniziro cha Mulungu analenga munthu. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+