Danieli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Palibe amuna anzeru, anthu olankhula ndi mizimu, ansembe ochita zamatsenga kapena anthu okhulupirira nyenyezi amene angakwanitse kukuuzani inu mfumu chinsinsi chimene mukufuna kudziwa.+ Danieli 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imeneyo ansembe ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi okhulupirira nyenyezi+ anabwera kwa ine. Nditawafotokozera malotowo, sanathe kundiuza kumasulira kwake.+
27 Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Palibe amuna anzeru, anthu olankhula ndi mizimu, ansembe ochita zamatsenga kapena anthu okhulupirira nyenyezi amene angakwanitse kukuuzani inu mfumu chinsinsi chimene mukufuna kudziwa.+
7 Pa nthawi imeneyo ansembe ochita zamatsenga, anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi okhulupirira nyenyezi+ anabwera kwa ine. Nditawafotokozera malotowo, sanathe kundiuza kumasulira kwake.+