Danieli 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kumwamba kuli Mulungu amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani inu Mfumu Nebukadinezara zimene zidzachitike mʼmasiku otsiriza. Maloto anu komanso masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa: Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonseAsanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
28 Koma kumwamba kuli Mulungu amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani inu Mfumu Nebukadinezara zimene zidzachitike mʼmasiku otsiriza. Maloto anu komanso masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa:
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonseAsanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+