Genesis 46:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yosefe anabereka Manase+ ndi Efuraimu+ ku Iguputo. Anabereka anawa ndi mkazi wake Asenati+ mwana wa Potifera, wansembe wa mzinda wa Oni.*
20 Yosefe anabereka Manase+ ndi Efuraimu+ ku Iguputo. Anabereka anawa ndi mkazi wake Asenati+ mwana wa Potifera, wansembe wa mzinda wa Oni.*