Machitidwe 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Yakobo anamva kuti ku Iguputo kuli chakudya, ndipo anatuma makolo athu aja kwa nthawi yoyamba.+
12 Koma Yakobo anamva kuti ku Iguputo kuli chakudya, ndipo anatuma makolo athu aja kwa nthawi yoyamba.+