-
Genesis 45:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ana a Isiraeli aja anachitadi zimenezo. Yosefe anawapatsa ngolo monga momwe Farao analamulira. Anawapatsanso chakudya cha pa ulendo.
-
-
Genesis 45:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Kwa bambo ake anatumizako abulu 10 onyamula zinthu zabwino zochokera ku Iguputo, abulu aakazi 10 onyamula tirigu ndi chakudya chawo cha pa ulendo.
-