Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pamene amalonda a Chimidiyani+ aja ankadutsa, abale a Yosefe anamutulutsa mʼchitsimemo nʼkumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo amalondawo anapita naye ku Iguputo.

  • Genesis 37:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ana ake onse aamuna ndi aakazi ankapita kukamutonthoza, koma iye ankakana kutonthozedwa. Ankanena kuti: “Ayi! Ndidzalira mpaka kutsikira ku Manda*+ kumene kuli mwana wanga.” Ndipo bambo akewo anapitiriza kumulira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena