-
Genesis 47:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Chakacho chitatha, anthu anayamba kupita kwa iye chaka chotsatira. Iwo ankanena kuti: “Tisakubisireni mbuyathu, ndalama zathu ndi ziweto zonse zatha chifukwa tinazipereka kwa inu. Tilibenso chilichonse choti tikupatseni kupatulapo matupi athuwa komanso minda yathu.
-