Genesis 46:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yosefe anauza anthu kuti amukonzere galeta lake, kenako ananyamuka kuti akakumane ndi Isiraeli bambo ake ku Goseni. Atangofika kwa bambo akewo, nthawi yomweyo anawakumbatira nʼkulira kwa kanthawi.*
29 Yosefe anauza anthu kuti amukonzere galeta lake, kenako ananyamuka kuti akakumane ndi Isiraeli bambo ake ku Goseni. Atangofika kwa bambo akewo, nthawi yomweyo anawakumbatira nʼkulira kwa kanthawi.*