Genesis 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Madziwo anakwera kwambiri kupitirira mapiriwo ndi mamita pafupifupi 6 ndi hafu.*