Genesis 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu atatero, anazidalitsa ponena kuti: “Muswane ndipo muchulukane nʼkudzaza nyanja zonse.+ Ndipo zamoyo zouluka zichuluke padziko lapansi.”
22 Mulungu atatero, anazidalitsa ponena kuti: “Muswane ndipo muchulukane nʼkudzaza nyanja zonse.+ Ndipo zamoyo zouluka zichuluke padziko lapansi.”