19 Ndiyeno Yehova Mulungu anaumba ndi dothi nyama iliyonse yakutchire komanso chamoyo chilichonse chouluka mumlengalenga ndipo anazipititsa kwa munthuyo kuti azipatse mayina. Dzina lililonse limene munthuyo anapatsa chamoyo chilichonse linakhaladi dzina lake.+