Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+ Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita zinthu zopanda chilungamo.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 104:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+ Zonsezo munazipanga mwanzeru.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga. 1 Timoteyo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa chilichonse cholengedwa ndi Mulungu nʼchabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati munthu wayamika Mulungu pakudya,
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+ Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita zinthu zopanda chilungamo.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+ Zonsezo munazipanga mwanzeru.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.
4 Chifukwa chilichonse cholengedwa ndi Mulungu nʼchabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati munthu wayamika Mulungu pakudya,