Genesis 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano Yehova Mulungu anatenga munthu uja nʼkumuika mʼmunda wa Edeni kuti aziulima komanso kuusamalira.+ Genesis 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atatero Yehova Mulungu anatulutsa munthuyo mʼmunda wa Edeni,+ kuti akalime nthaka imene anatengedwako.+
15 Tsopano Yehova Mulungu anatenga munthu uja nʼkumuika mʼmunda wa Edeni kuti aziulima komanso kuusamalira.+
23 Atatero Yehova Mulungu anatulutsa munthuyo mʼmunda wa Edeni,+ kuti akalime nthaka imene anatengedwako.+