Aheberi 6:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu, analumbira pa dzina lake chifukwa panalibe wina wamkulu kuposa iyeyo amene akanamulumbirira.+ 14 Iye anati: “Ndithudi ndidzakudalitsa ndipo ndidzachulukitsa mbadwa zako.”+
13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu, analumbira pa dzina lake chifukwa panalibe wina wamkulu kuposa iyeyo amene akanamulumbirira.+ 14 Iye anati: “Ndithudi ndidzakudalitsa ndipo ndidzachulukitsa mbadwa zako.”+