-
Genesis 13:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Abulamu atasiyana ndi Loti, Yehova anamuuza kuti: “Takweza maso ako kuchokera pamene ulipo. Uyangʼane kumpoto ndi kumʼmwera, komanso kumʼmawa ndi kumadzulo.
-