Genesis 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzaika chidani+ pakati pa iwe+ ndi mkaziyo,+ komanso pakati pa mbadwa* yako+ ndi mbadwa yake.+ Mbadwa ya mkaziyo idzaphwanya mutu wako,+ ndipo iwe udzaivulaza chidendene.”+ Aroma 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso sikuti onse ndi ana chifukwa choti ndi mbadwa* za Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+ Agalatiya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano malonjezo anaperekedwa kwa Abulahamu ndi kwa mbadwa yake.*+ Malemba sanena kuti: “Kwa mbadwa zako,”* ngati kuti mbadwazo nʼzambiri. Koma akunena kuti, “kwa mbadwa yako,”* kutanthauza kuti ndi imodzi, amene ndi Khristu.+
15 Ndidzaika chidani+ pakati pa iwe+ ndi mkaziyo,+ komanso pakati pa mbadwa* yako+ ndi mbadwa yake.+ Mbadwa ya mkaziyo idzaphwanya mutu wako,+ ndipo iwe udzaivulaza chidendene.”+
7 Ndiponso sikuti onse ndi ana chifukwa choti ndi mbadwa* za Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+
16 Tsopano malonjezo anaperekedwa kwa Abulahamu ndi kwa mbadwa yake.*+ Malemba sanena kuti: “Kwa mbadwa zako,”* ngati kuti mbadwazo nʼzambiri. Koma akunena kuti, “kwa mbadwa yako,”* kutanthauza kuti ndi imodzi, amene ndi Khristu.+