Genesis 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tera anakhala ndi moyo zaka 70, kenako anabereka Abulamu,+ Nahori+ ndi Harana. Genesis 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Abulamu ndi Nahori anakwatira. Mkazi wa Abulamu anali Sarai,+ pamene mkazi wa Nahori anali Milika,+ mwana wa Harana. Harana analinso bambo ake a Yisika.
29 Abulamu ndi Nahori anakwatira. Mkazi wa Abulamu anali Sarai,+ pamene mkazi wa Nahori anali Milika,+ mwana wa Harana. Harana analinso bambo ake a Yisika.