Yoswa 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Poyamba mzinda wa Heburoni unkatchedwa Kiriyati-ariba.+ (Ariba anali munthu wamphamvu pakati pa Aanaki.) Kenako mʼdzikolo munakhala mopanda nkhondo.+
15 Poyamba mzinda wa Heburoni unkatchedwa Kiriyati-ariba.+ (Ariba anali munthu wamphamvu pakati pa Aanaki.) Kenako mʼdzikolo munakhala mopanda nkhondo.+