Genesis 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Ndimvereni mbuyanga. Malowo mtengo wake ndi siliva wolemera masekeli 400.* Koma ndalamazo si nkhani yaikulu pakati pa ine ndi inu. Kaikeni malemuwo.”
15 “Ndimvereni mbuyanga. Malowo mtengo wake ndi siliva wolemera masekeli 400.* Koma ndalamazo si nkhani yaikulu pakati pa ine ndi inu. Kaikeni malemuwo.”