Genesis 11:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mbiri ya Tera ndi iyi. Tera anabereka Abulamu, Nahori ndi Harana. Harana anabereka Loti.+ 28 Pambuyo pake, Harana anamwalira mumzinda wa Uri+ womwe ndi wa Akasidi,+ kumene anabadwira. Anamwalira bambo ake Tera ali ndi moyo. Genesis 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anamuuzanso kuti: “Ine ndine Yehova, amene ndinakuchotsa ku Uri, mzinda wa Akasidi, kuti ndidzakupatse dzikoli likhale lako.”+
27 Mbiri ya Tera ndi iyi. Tera anabereka Abulamu, Nahori ndi Harana. Harana anabereka Loti.+ 28 Pambuyo pake, Harana anamwalira mumzinda wa Uri+ womwe ndi wa Akasidi,+ kumene anabadwira. Anamwalira bambo ake Tera ali ndi moyo.
7 Anamuuzanso kuti: “Ine ndine Yehova, amene ndinakuchotsa ku Uri, mzinda wa Akasidi, kuti ndidzakupatse dzikoli likhale lako.”+