Aheberi 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma akanakhala kuti ankangoganizira za kumene anachokera,+ akanapeza chifukwa chowapangitsa kuti abwerere.
15 Koma akanakhala kuti ankangoganizira za kumene anachokera,+ akanapeza chifukwa chowapangitsa kuti abwerere.