Genesis 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Abulamu anatenga mkazi wake Sarai,+ Loti mwana wa mʼbale+ wake ndi chuma chawo chonse+ komanso akapolo awo onse amene anapeza kudziko la Harana. Iwo ananyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani.+ Atafika ku Kanani,
5 Abulamu anatenga mkazi wake Sarai,+ Loti mwana wa mʼbale+ wake ndi chuma chawo chonse+ komanso akapolo awo onse amene anapeza kudziko la Harana. Iwo ananyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani.+ Atafika ku Kanani,