-
Genesis 29:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Yakobo ataona Rakele mwana wa Labani, mchimwene wa mayi ake, ndiponso nkhosa za Labaniyo, nthawi yomweyo anapita pachitsime paja nʼkugubuduza mwalawo kuuchotsa pachitsimepo. Atatero anatungira madzi nkhosa za Labani, mchimwene wa mayi ake.
-