Genesis 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatero, mtumikiyo anaika dzanja lake pansi pa ntchafu ya Abulahamu mbuye wake nʼkulumbira kwa iye pa nkhani imeneyi.+
9 Atatero, mtumikiyo anaika dzanja lake pansi pa ntchafu ya Abulahamu mbuye wake nʼkulumbira kwa iye pa nkhani imeneyi.+