Genesis 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Patapita nthawi, Abimeleki mfumu ya Afilisiti ankayangʼana pawindo, ndipo anaona Isaki akucheza mwachikondi ndi mkazi wake* Rabeka.+
8 Patapita nthawi, Abimeleki mfumu ya Afilisiti ankayangʼana pawindo, ndipo anaona Isaki akucheza mwachikondi ndi mkazi wake* Rabeka.+