Genesis 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, kenako Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni. Genesis 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a Isakara anali Tola, Puva, Yabi ndi Simironi.+ Genesis 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Isakara+ ndi bulu wa mafupa olimba. Amagona pansi kuti apume, atanyamula matumba awiri a katundu. Deuteronomo 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ponena za Zebuloni anati:+ “Kondwera Zebuloni iwe, pa maulendo ako,Ndiponso iwe Isakara, mʼmatenti ako.+
23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, kenako Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni.
18 Ponena za Zebuloni anati:+ “Kondwera Zebuloni iwe, pa maulendo ako,Ndiponso iwe Isakara, mʼmatenti ako.+