Genesis 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Dina, mwana wamkazi amene Leya anaberekera Yakobo,+ ankakonda kukacheza ndi* atsikana a mumzindawo.+
34 Dina, mwana wamkazi amene Leya anaberekera Yakobo,+ ankakonda kukacheza ndi* atsikana a mumzindawo.+