Genesis 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndili ndi iwe. Ndikuyangʼanira kulikonse kumene ungapite ndipo ndidzakubwezera kudziko lino.+ Sindidzakusiya mpaka nditachita zimene ndakulonjeza.”+ Genesis 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ kumene unadzoza mwala wachikumbutso kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+
15 Ine ndili ndi iwe. Ndikuyangʼanira kulikonse kumene ungapite ndipo ndidzakubwezera kudziko lino.+ Sindidzakusiya mpaka nditachita zimene ndakulonjeza.”+
13 Ndine Mulungu woona wa ku Beteli+ kumene unadzoza mwala wachikumbutso kuja, kumenenso unachita lonjezo kwa ine.+ Tsopano nyamuka, uchoke kudziko lino, ubwerere kudziko limene unabadwira.’”+