Genesis 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nthawi zonse akanena kuti, ‘Zamawangamawanga ndi zimene zidzakhale malipiro ako,’ ziweto zonse zinkabereka zamawangamawanga. Akanena kuti, ‘Zamizeremizere ndi zimene zidzakhale malipiro ako,’ ziweto zonse zinkabereka zamizeremizere.+
8 Nthawi zonse akanena kuti, ‘Zamawangamawanga ndi zimene zidzakhale malipiro ako,’ ziweto zonse zinkabereka zamawangamawanga. Akanena kuti, ‘Zamizeremizere ndi zimene zidzakhale malipiro ako,’ ziweto zonse zinkabereka zamizeremizere.+