Genesis 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mʼchaka cha 600 cha moyo wa Nowa, mʼmwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli madzi onse akumwamba anaphulika ndipo zitseko zotchingira madzi akumwamba zinatseguka.+ Miyambo 8:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene ankakonza kumwamba, ine ndinali pomwepo.+Pamene ankaika malire pakati pa mlengalenga ndi nyanja,+28 Pamene ankakhazikitsa* mitambo kumwamba,Pamene ankakhazikitsa akasupe a madzi akuya,
11 Mʼchaka cha 600 cha moyo wa Nowa, mʼmwezi wachiwiri,* pa tsiku la 17 la mweziwo, pa tsiku limeneli madzi onse akumwamba anaphulika ndipo zitseko zotchingira madzi akumwamba zinatseguka.+
27 Pamene ankakonza kumwamba, ine ndinali pomwepo.+Pamene ankaika malire pakati pa mlengalenga ndi nyanja,+28 Pamene ankakhazikitsa* mitambo kumwamba,Pamene ankakhazikitsa akasupe a madzi akuya,