Genesis 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chonde ndipulumutseni+ mʼdzanja la mchimwene wanga, Esau. Ndikuchita naye mantha kuti akafika, akhoza kundivulaza+ komanso kuvulaza akaziwa limodzi ndi ana awo. Genesis 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mukamuuzenso kuti, ‘Ndiponso kapolo wanu Yakobo ali mʼmbuyo mwathumu.’” Popeza mumtima mwake anati: “Ngati angasangalale ndi mphatso imene ndatumizayi,+ ndiye kuti ndikakumana naye akhoza kundilandira bwino.”
11 Chonde ndipulumutseni+ mʼdzanja la mchimwene wanga, Esau. Ndikuchita naye mantha kuti akafika, akhoza kundivulaza+ komanso kuvulaza akaziwa limodzi ndi ana awo.
20 Mukamuuzenso kuti, ‘Ndiponso kapolo wanu Yakobo ali mʼmbuyo mwathumu.’” Popeza mumtima mwake anati: “Ngati angasangalale ndi mphatso imene ndatumizayi,+ ndiye kuti ndikakumana naye akhoza kundilandira bwino.”