Yoswa 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Yoswa anasonkhanitsa mafuko onse a Isiraeli ku Sekemu. Iye anaitanitsa akulu a Isiraeli, atsogoleri, oweruza ndi akapitawo+ ndipo onse anaima pamaso pa Mulungu woona.
24 Kenako Yoswa anasonkhanitsa mafuko onse a Isiraeli ku Sekemu. Iye anaitanitsa akulu a Isiraeli, atsogoleri, oweruza ndi akapitawo+ ndipo onse anaima pamaso pa Mulungu woona.